|
2.
|
|
|
To encrypt your home directory or "Private" folder, a strong passphrase has been automatically generated. Usually your directory is unlocked with your user password, but if you ever need to manually recover this directory, you will need this passphrase. Please print or write it down and store it in a safe location. If you click "Run this action now", enter your login password at the "Passphrase" prompt and you can display your randomly generated passphrase. Otherwise, you will need to run "ecryptfs-unwrap-passphrase" from the command line to retrieve and record your generated passphrase.
|
|
|
Description
|
|
|
|
Kuti mubise home directory kapena malo anu a "Private", mawu alimba apangidwa kale okha. Nthawi zambiri malowa adzitsegulidwa mukalowetsa liwu lanu lachinsisi lanthawi zonse, koma ngati mungadzafune kusintha nokha liwuli, mudzafunika mukhale nalo panthiwiyo. Chonde lembani dzinali penapake ndikulisunga pamalo abwino. Mukatobwanya "Run this action now", lowetsani dzina lachinsisi pamalo olemba "Passphrase" ndipo mutha kuona liwu lachinsisi lopangidwa lokha. Kupanda apo, pafunika mupange "encryptfs-unwarap-passphrase" kuchokela kumalo olemba mawu okha okha kuti muthe kutenga liwu lanu lachinsisi.
|
|
Translated and reviewed by
Herald Luwizghie
|
|
|
|
Located in
../src/desktop/ecryptfs-record-passphrase:8
|
|
3.
|
|
|
Access Your Private Data
|
|
|
|
Onani uthenga wanu wobisika
|
|
Translated and reviewed by
Herald Luwizghie
|
|
|
|
Located in
../src/desktop/ecryptfs-mount-private.desktop.in.h:1
|
|
4.
|
|
|
Setup Your Encrypted Private Directory
|
|
|
|
Khonzekeletsani malo anu achinsinsi
|
|
Translated and reviewed by
Herald Luwizghie
|
|
|
|
Located in
../src/desktop/ecryptfs-setup-private.desktop.in.h:1
|