Translations by Herald Luwizghie

Herald Luwizghie has submitted the following strings to this translation. Contributions are visually coded: currently used translations, unreviewed suggestions, rejected suggestions.

112 of 12 results
1.
Monitor Resolution Settings has detected that the virtual resolution must be set in your configuration file in order to apply your settings. Would you like Screen Resolution to set the virtual resolution for you? (Recommended)
2015-03-09
Monitor Resolution Settings yaona kuti maonekedwe ake akuyenela kupangidwa ndiinu eni mufailo yosungilamo zokhodza magwilidwe ntchito a kompyuta iyi kuti ithe kukhazikitsa maonekedwe awa. Mungafune Screen Resolution ikusinthileni maonekedwewa? (Zovemelezeka)
2.
Could not connect to Monitor Resolution Settings DBUS service.
2015-03-09
Zakanika kulumikizana ndi Monito Resolution Setteings DBUS service.
3.
Please log out and log back in again. You will then be able to use Monitor Resolution Settings to setup your monitors
2015-03-16
Chonde tulukani ndiye mulowenso. Mudzatha kugwilitsa ntchito Monito Resolution Settings kukhonza sikilini yanu.
2015-03-09
Chonde tulukani ndiye mulowenso.
4.
Monitor Resolution Settings can't apply your settings.
2015-03-16
Monitor Resolution Settings ikukanika kukhzazikitsa zokhonza zanu.
5.
Monitor Resolution Settings
2015-03-16
Monitor Resolution Settings
6.
Change Screen Resolution Configuration
2015-03-16
Sinthani maonekedwe a sikilini yanu.
7.
Changing the Screen Resolution configuration requires privileges.
2015-03-16
Kusintha maonekedwe a sikilini yanu zifunika kuvomelezedwa ndiwoyenelela.
8.
Change the effect of Ctrl+Alt+Backspace
2015-03-16
Sinthani zoonjezelazi po tobwanya Ctrl+Alt+Backspace
9.
Changing the effect of Ctrl+Alt+Backspace requires privileges.
2015-03-16
kusintha zoonjezelazi po tobwanya Ctrl+Alt+Backspace zifunika kuvomelezedwa ndiwoyenelela.
10.
Enable or disable the NVIDIA GPU with PRIME
2015-03-16
Lolezani kapena letsani NVIDIA GPU ndi PRIME
11.
Enabling or disabling the NVIDIA GPU requires privileges.
2015-03-09
Kuloleza kapena kulepheletsa NVIDIA GPU kufuna chilolezo.